Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Zeresi mkazi wace, ndi mabwenzi ace onse ananena naye, Apange mtengo, msinkhu wace mikono makumi asanu, ndi mawa mukanene nayo mfumu kuti ampacike Moredekai pamenepo; nimulowe pamodzi ndi mfumu kumadyerero wokondwera. Ndipo ici cidakomera Hamani, napangitsa anthu mtengowo.

Werengani mutu wathunthu Estere 5

Onani Estere 5:14 nkhani