Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Hamani anatinso, Ndiponso Estere mkazi wamkuru sanalola mmodzi yense alowe pamodzi ndi mfumu ku madyerero adakonzawo, koma ine ndekha; nandiitana mawanso pamodzi ndi mfumu.

Werengani mutu wathunthu Estere 5

Onani Estere 5:12 nkhani