Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 4:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Muka, sonkhanitsa Ayuda onse opezeka m'Susani, nimundisalire, osadya osamwa masiku atatu, usiku ndi usana, ine ndemwe ndi anamwali anga tidzasala momwemo, ndipo motero ndidzalowa kwa mfumu, ndiko kosalingana ndi lamulo; ndikaonongeka tsono ndionongeke,

Werengani mutu wathunthu Estere 4

Onani Estere 4:16 nkhani