Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 4:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma podziwa Moredekai zonse zidacitikazi, Moredekai anang'amba zobvala zace, nabvala ciguduli ndi mapulusa, naturuka pakati pa mudzi, napfuula, nalira kulira kwakukuru ndi kowawa,

Werengani mutu wathunthu Estere 4

Onani Estere 4:1 nkhani