Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 3:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cikakomera mfumu, cilembedwe kuti aonongeke iwo; ndipo ndidzapereka matalente a siliva zikwi khumi m'manja a iwo akusunga nchito ya mfumu, abwere nao kuwaika m'nyumba za cuma ca mfumu.

Werengani mutu wathunthu Estere 3

Onani Estere 3:9 nkhani