Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anaciyesa copepuka kumthira manja Moredekai yekha; pakuti adamfotokozera mtundu wace wa Moredekai; potero Hamani anafuna kuononga Ayuda lonse okhala m'ufumu wonse wa Ahaswero, ndiwo a mtundu wa Moredekai.

Werengani mutu wathunthu Estere 3

Onani Estere 3:6 nkhani