Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 3:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatumiza akalata ndi amtokoma ku maiko onse a mfumu, kuti aononge, aphe, napulule Ayuda onse, ndiwo ana, ndi okalamba, makanda, ndi akazi, tsiku limodzi, ndilo tsiku lakhumi ndi citatu la mwezi wakhumi ndi ciwiri, ndiwo mwezi wa Adara; nalande zao mofunkha.

Werengani mutu wathunthu Estere 3

Onani Estere 3:13 nkhani