Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi mfumu aike oyang'anira m'maiko onse a ufumu wace, kuti asonkhanitse anamwali onse okongola m'cinyumba ca ku Susani, m'nyumba ya akazi; awasunge Hege mdindo wa mfumu wosungira akazi, nawapatse zowayeretsa;

Werengani mutu wathunthu Estere 2

Onani Estere 2:3 nkhani