Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 2:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inakonda Estere koposa akazi onse, nalandira iye kuyanja ndi cifundo pamaso pace, koposa anamwali onse; motero anaika korona wacifumu pamutu pace, namuyesa mkazi wamkuru m'malo mwa Vasiti.

Werengani mutu wathunthu Estere 2

Onani Estere 2:17 nkhani