Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 2:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pofika tsono kulowa kwace kwa Estere mwana wa Abihaili, atate wamng'ono wa Moredekai, amene adadzitengera akhale mwana wace, kuti alowe kwa mfumu, sanafuna kanthu koma zonena Hege mdindo wa mfumu wosunga akazi ndizo. Ndipo Estere anayamikizidwa pamaso pa onse ompenya.

Werengani mutu wathunthu Estere 2

Onani Estere 2:15 nkhani