Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 2:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunafika tsono kulowa kwace kwa namwali ali yense, kuti alowe kwa mfumu Ahaswero, atamcitira monga mwa lamulo la akazi, miyezi khumi ndi iwiri; pakuti adafokwaniritsa masiku a mayeretsedwe ao motero, miyezi isanu ndi umodzi ndi mafuta a mure, ndi miyezi isanu ndi umodzi ndi zonunkhira bwino, ndi zoyeretsa akazi.

Werengani mutu wathunthu Estere 2

Onani Estere 2:12 nkhani