Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 1:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatha masikuwa, mfumu inakonzera madyerero anthu onse okhala m'cinyumba ca ku Susani, akulu ndi ang'ono, masiku asanu ndi awiri, ku bwalo la munda wa maluwa wa ku cinyumba ca mfumu;

Werengani mutu wathunthu Estere 1

Onani Estere 1:5 nkhani