Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Vasiti mkazi wamkuruyo anakana kudza pa mau a mfumu adamuuza adindowo; potero mfumu idapsa mtima ndithu, ndi mkwiyo wace unatentha m'kati mwace.

Werengani mutu wathunthu Estere 1

Onani Estere 1:12 nkhani