Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Estere 1:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

IZI zinacitika masiku a Ahaswero, ndiye Ahasweroyo anacita ufumu kuyambira Indiya kufikira Kusi, pa maiko zana limodzi mphambu makumi awiri kudza asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu Estere 1

Onani Estere 1:1 nkhani