Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 9:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo lidzakhala pfumbi losalala pa dziko lonse la Aigupto, ndipo lidzakhala pa anthu ndi pa zoweta ngati zironda zobuka ndi matuza, m'dziko lonse la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 9

Onani Eksodo 9:9 nkhani