Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 9:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yehova anati kwa Mose, Lowa kwa Farao, numuuze, Atero Yehova Mulungu wa Ahebri, Lola anthu anga amuke, kuti anditumikire.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 9

Onani Eksodo 9:1 nkhani