Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Mose anati kwa Farao, Ulemu ndi wanu, wa ine ai; ndipembere inu ndi anyamata anu ndi anthu anu liti, kuti aonongeke aculewo, acokere inu ndi nyumba zanu, atsale m'nyanja mokha?

Werengani mutu wathunthu Eksodo 8

Onani Eksodo 8:9 nkhani