Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 8:31-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. Ndipo Yehova anacita monga mwa mau a Mose; nacotsera Farao ndi anyamata ace ndi anthu ace mizazayo, sunatsala ndi umodzi wonse.

32. Koma Farao anaumitsa mtima wace nthawi yomweyonso, ndipo sanalola anthu amuke.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 8