Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo m'nyanjamo mudzacuruka acule, amene adzakwera nadzalowa m'nyumba mwako, ndi m'cipinda cogona iwe, ndi pakama pako, ndi m'nyumba ya anyamata ako, ndi pa anthu ako, m'micembo yanu yooceramo, ndi m'mbale zanu zoumbiramo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 8

Onani Eksodo 8:3 nkhani