Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Farao adzalankhula nanu, ndi kuti, Dzicitireni codabwiza; pamenepo uzinena ndi Aroni, Tenga ndodo yako, Iponye pansi pamaso pa Farao, isanduke cinjoka,

Werengani mutu wathunthu Eksodo 7

Onani Eksodo 7:9 nkhani