Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 7:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova ananena ndi Mose, Taona, ndakuika ngati Mulungu kwa Farao; ndi Aroni mkuru wako adzakhala mneneri wako.

2. Iwe uzdankhula zonse ndikulamulira; ndi Aroni mkuru wako azilankhula kwa Farao, kuti alole ana a Israyeli aturuke m'dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 7