Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 6:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Awa ndi omwewo ananena ndi Farao, mfumu ya Aigupto, awaturutse ana a Israyeli m'Aigupto; Mose ndi Aroni amenewa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 6

Onani Eksodo 6:27 nkhani