Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 6:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eleazara mwana wa Aroni anadzitengera mkazi wa ana akazi a Putieli akhale mkazi wace, ndipo anambalira Pinehasi. Amenewo ndi akuru a makolo a Alevi mwa mabanja ao.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 6

Onani Eksodo 6:25 nkhani