Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 6:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aroni anadzitengera Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mlongo wace wa Nasoni, akhale mkazi wace; ndipo anambalira Nadabu ndi Abihu, Eleazara ndi ltamara.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 6

Onani Eksodo 6:23 nkhani