Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nawalangiza za ana a Israyeli, ndi za Farao mfumu ya Aigupto, kuti aturutse ana a Israyeli m'dziko la Aigupto.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 6

Onani Eksodo 6:13 nkhani