Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 5:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ananena nao, Yehova akupenyeni, naweruze; pakuti mwatinyansitsa pamaso pa Farao, ndi pamaso pa anyamata ace, ndi kuwapatsa lupanga m'dzanja lao kutipha nalo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 5

Onani Eksodo 5:21 nkhani