Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 40:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti,

2. Tsiku loyamba la mwezi woyamba ukautse kacisi wa cihema cokomanako.

3. Ndipo ukaikemo likasa la mboni, nucinge likasalo ndi nsaru yocingayo.

4. Ulongenso gomelo, nukonzerepo zokonzera zace; ulongenso coikapo nyalico, ndi kuyatsa nyali zace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 40