Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 4:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananenanso naye, Longa dzanja lako pacifuwa pako. Ndipo analonga dzanja lace pacifuwa pace, naliturutsa, taonani, dzanja lace linali lakhate, lotuwa ngati cipale cofewa.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 4

Onani Eksodo 4:6 nkhani