Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 4:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova ananena ndi Aroni, Muka kucipululu kukakomana ndi Mose. Ndipo anamuka, nakomana naye pa phiri la Mulungu, nampsompsona.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 4

Onani Eksodo 4:27 nkhani