Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nsaru zocingira za pabwalo, osici zace, ndi makamwa ace, ndi nsaru yotsekera pa cipata ca pabwalo, zingwe zace, ndi ziciri zace, ndi zipangizo zonse za nchito ya kacisi, za ku cihema cokomanako;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:40 nkhani