Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anabwera naye kacisi kwa Mose, cihemaco, ndi zipangizo zace zonse, zokowera zace, matabwa ace, mitanda yace, ndi mizati yace, nsanamira zace ndi nsici zace, ndi makamwa ace;

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:33 nkhani