Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 39:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo miyalayi inakhala monga mwa maina a ana a Israyeli, khumi ndi awiri, monga mwa maina ao; ngati malocedwe a cosindikizira, yonse monga mwa maina ace, kwa mafuko khumi ndi awiriwo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 39

Onani Eksodo 39:14 nkhani