Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 38:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga zokowera za mizati nsanamira ndi nsici ndi masekeli aja cikwi cimodzi kudza mazana asanu ndi awiri mphambu asanu, nakuta mitu yace, nazigwirizitsana pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 38

Onani Eksodo 38:28 nkhani