Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 38:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ici ndi ciwerengo ca zinthu za cihema, cihema ca mboni, monga anaziwerenga, monga mwa mau a Mose, acite nazo Alevi; anaziwerenga Itamara, mwana wa Aroni wansembe.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 38

Onani Eksodo 38:21 nkhani