Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 38:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi nsaru yotsekera pa cipata ca pabwalo ndiyo nchito ya wopikula, ya lamadzi, ndi lofiirira, ndi lofiira, ndi bafuta wa thonje losansitsa; utali wace mikono makumi awiri, ndi msinkhu wace mu kupingasa kwace mikono isanu, yolingana ndi nsaru zocingira za pabwalo.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 38

Onani Eksodo 38:18 nkhani