Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 38:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pa mbali ya kumadzulo panali nsaru zocingira za mikono makumi asanu, nsid zace khumi, ndi makamwa ace khumi; zokowera za nsici ndi mitanda yace yasiliva.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 38

Onani Eksodo 38:12 nkhani