Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 37:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akerubi anafunyulira mapiko ao m'mwamba, ndi kuphimba cotetezerapo ndi mao piko ao, ndi nkhope zao zopeoyana; zinapenya kucotetezerapo nkhope zao.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 37

Onani Eksodo 37:9 nkhani