Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 36:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

napanga makamwa makumi anai pansi pamatabwa makumi awiri; makamwa awiri pansi pa thabwa limodzi kwa mitsukwa yace iwiri, ndi makamwa awiri pansi pa thabwa lina kwa mitsukwa yace iwiri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:24 nkhani