Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 36:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anapanga magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru imodzi, ya kuthungo, ya cilumikizano, naika magango makumi asanu m'mphepete mwa nsaru ya kuthungo, ya cilumikizano cina.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 36

Onani Eksodo 36:17 nkhani