Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 35:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yense wakupereka copereka ca siliva ndi mkuwa, anabwera naco copereka ca Yehova; ndi yense amene kwao kunapezeka mtengo wasitimu wa ku macitidwe onse a nchitoyi, anabwera nao.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 35

Onani Eksodo 35:24 nkhani