Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 34:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma woyamba wa buru uzimuombola ndi mwana wa nkhosa; ukapanda kumuombola, uzimthyola khosi. Ana anu amuna oyamba onse uziwaombola. Ndipo asamaoneka pamaso panga opanda kanthu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 34

Onani Eksodo 34:20 nkhani