Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 32:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace anauka mamawa, nafukiza nsembe zopsereza, nabwera nazo nsembe zamtendere; ndi anthu anakhala pansi kudya ndi kumwa, nauka kusewera.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 32

Onani Eksodo 32:6 nkhani