Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 32:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ananena nao, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Yense amange lupanga lace m'cuuno mwace, napite, nabwerere kuyambira cipata kufikira cipata, pakati pa cigono, naphe yense mbale wace, ndi yense bwenzi lace, ndi yense mnansi wace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 32

Onani Eksodo 32:27 nkhani