Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 32:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pamene anayandikiza cigono, anaona mwana wa ng'ombeyo ndi kubvinako; ndipo Mose anapsa mtima, nataya magome ali m'manja mwace, nawaswa m'tsinde mwa phiri.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 32

Onani Eksodo 32:19 nkhani