Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 32:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma pamene anaona kuti Mose anacedwa kutsika m'phiri, anthuwo anasonkhana kwa Aroni, nanena naye, Ukani, tipangireni milungu yakutitsogolera; pakuti Mose uyu, munthuyu anatikweza kucokera m'dziko la Aigupto, sitidziwa comwe camgwera.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 32

Onani Eksodo 32:1 nkhani