Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 31:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muzisunga Sabata; popeza ndilo lopatulika la kwa inu; ali yense wakuliipsa aphedwe ndithu; pakuti ali yense wakugwira nchito m'mwemo, munthu ameneyo asadzidwe mwa anthu a mtundu wace.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 31

Onani Eksodo 31:14 nkhani