Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 30:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Aroni azicita coteteza pa nyanga zace kamodzi m'caka; alicitire coteteza ndi mwazi wa nsembe yaucimo ya coteteza, mwa mibadwo yanu; ndilo lopatulikitsa la Yehova.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 30

Onani Eksodo 30:10 nkhani