Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndatsikira kuwalanditsa m'manja a anthu a Aigupto, ndi kuwatumtsa m'dziko lila akwere nalowe m'dziko labwino ndi lalikuru, m'dziko moyenda mkaka ndi uci ngati madzi; ku malo a Akanani, ndi Ahiti ndi Aamori, ndi Aperizi, ndi Ahivi, ndi Ayebusi.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:8 nkhani