Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 3:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzamveca mau ako; ndipo ukapite iwe ndi akuru a Israyeli, kwa mfumu ya Aigupto, ndi kukanena naye, Yehova, Mulungu wa Ahebri wakomana ndi ife; tiloleni, timuke tsopano ulendo wa masiku atatu m'cipululu, kuti timphere nsembe Yehova Mulungu wathu.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 3

Onani Eksodo 3:18 nkhani