Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Eksodo 29:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo adzadziwa kuti Ine ndine Yehova Mulungu wao, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto, kuti ndikhale pakati pao. Ine ndine Yehova Mulungu wao.

Werengani mutu wathunthu Eksodo 29

Onani Eksodo 29:46 nkhani